YESAYA 29-33
CUMA COCOKELA M’MAU A MULUNGU |“Mfumu Idzalamulila Mwacilungamo”
Mfumu Yesu, waika “akalonga,” amene ni akulu, kuti asamalile nkhosa
32:1-3
-
Mofanana ndi “malo ousapo mvula yamkuntho,” akulu amateteza nkhosa ku mazunzo na zinthu zolefula
-
Mofanana ndi “mitsinje yamadzi m’dziko lopanda madzi,” akulu amatsitsimula amene ali na ludzu lauzimu, mwa kuwapatsa coonadi coyela, cosasukuluka
-
Mofanana ndi “mthunzi wa thanthwe lalikulu m’dziko louma,” akulu amateteza nkhosa mwa kuzipatsa malangizo ndi kuzitsitsimula