January 15-21
MATEYU 6-7
Nyimbo 21 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Pitilizani Kufuna-funa Ufumu Coyamba”: (10 min.)
Mat. 6:10—Ufumu unachulidwa pa zinthu zoyambilila m’pemphelo la citsanzo, kuonetsa kuti ni wofunika kwambili (bhs peji 178 pala. 12)
Mat. 6:24—Sitingathe kukhala kapolo wa Mulungu ndi wa “Cuma” (“kapolo” mfundo younikila Mat. 6:24 nwtsty)
Mat. 6:33—Yehova adzapeleka zosoŵa za atumiki ake okhulupilika oika zinthu za Ufumu patsogolo mu umoyo wawo (“pitilizani kufunafuna,” “Ufumu,” “cake,” “cilungamo” mfundo zounikila pa Mat. 6:33 nwtsty; w16.07 peji 12 pala. 18)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Mat. 7:12—Kodi vesiyi ingatithandize bwanji pokonzekela mau oyambila ulaliki? (w14 5/1 mape. 16, 17 mapa. 14-16)
Mat. 7:28, 29—Kodi khamu la anthu linakhudzidwa bwanji na zimene Yesu anali kuphunzitsa? Nanga n’cifukwa ciani? (“linadabwa,” “kaphunzitsidwe kake,” “osati monga alembi awo” mfundo zounikila pa Mat. 7:28, 29 nwtsty)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mat. 6:1-18
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano a citsanzo. Yankhani pa zimene ambili m’gawo lanu amakonda kukamba posafuna kulalikidwa.
Ulendo Wobwelelako Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano a citsanzo. Munthu amene munamulalikila mwapeza palibe, koma mwapezapo m’bululu wake.
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (5 min.) Tambani na kukambilana vidiyoyi.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Lekani Kuda Nkhawa”: (15 min.) Kukambilana. Yambani mwa kutambitsa vidiyo yakuti Zimene Tikuphunzilapo pa Mafanizo a Yesu—Onetsetsani Mbalame ndi Maluŵa.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 4
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 132 na Pemphelo