January 29–February 4
MATEYU 10-11
Nyimbo 4 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Yesu Anali Kutsitsimula Anthu”: (10 min.)
Mat. 10:29, 30—Mau a Yesu otiuza kuti Yehova amatikonda aliyense payekha amatitsitsimula (“mpheta,” “kakhobidi kamodzi kocepa mphamvu,” “tsitsi lenilenilo la m’mutu mwanu amaliŵelenga” mfundo zounikila pa Mat. 10:29, 30,“Mpheta” zithunzi nwtsty)
Mat. 11:28—Kutumikila Yehova kumatsitsimula (“olemedwa,” “ndidzakutsitsimutsani” mfundo zounikila pa Mat. 11:28, nwtsty)
Mat. 11:29, 30—Kugonjela ulamulilo wa Yesu na citsogozo cake kumatsitsimula (“Senzani goli langa” mfundo younikila pa Mat. 11:29, nwtsty)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Mat. 11:2, 3—N’cifukwa ciani Yohane M’batizi anafunsa funso limeneli? (jy peji 96 pala. 2-3)
Mat. 11:16-19—Kodi mavesi amenewa atanthauza ciani? (jy peji 98 pala. 1-2)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mat. 11:1-19
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Onani Makambilano a Citsanzo
Ulendo Wobwelelako Wacitatu: (3 min. olo kucepelapo) Dzisankhileni mwekha lemba, na funso lokakambilana pa ulendo wotsatila.
Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) bhs mape. 45-46 mapa. 15-16—Itanilani munthuyo ku misonkhano.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Kutsitsimula “Ogwila Nchito Yolemetsa ndi Olemedwa”: (15 min.) Tambitsani vidiyoyi Pambuyo pake, kambilanani mafunso aya:
N’zocitika ziti zaposacedwa zimene zapangitsa ena kufunikila citsitsimutso?
Kodi Yehova na Yesu acita zotani kuti apeleke citsitsimutso kupitila m’gulu?
Kodi Malemba amatitsitsimutsa bwanji?
Kodi aliyense wa ise angacite ciani kuti azitsitsimutsa ena?
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 6, na bokosi pa peji 20
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 138 na Pemphelo