January 8-14
MATEYU 4-5
Nyimbo 82 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Zimene Tiphunzilapo pa Ulaliki wa Yesu wa pa Phili”: (10 min.)
Mat. 5:3—Munthu amakhala wodala ngati azindikila zosoŵa zake zauzimu. (“Odala,” “anthu amene amazindikila zosoŵa zawo zauzimu” mfundo zounikila pa Mat. 5:3 nwtsty)
Mat. 5:7—Munthu amakhala wodala ngati ni wacifundo (“acifundo” mfundo younikila pa Mat. 5:7 nwtsty)
Mat. 5:9—Munthu amakhala wodala ngati amabweletsa mtendele (“amene amabweletsa mtendele” mfundo younikila pa Mat. 5:9 nwtsty; w07 12/1 peji 17)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Mat. 4:9—Kodi Satana anayesa kunyengelela Yesu kuti acite ciani? (“kuŵelama kamodzi kokha” mfundo younikila pa Mat. 4:9 nwtsty)
Mat. 4:23—Ni zinthu ziŵili ziti zofunika zimene Yesu anacita? (“kuphunzitsa . . . kulalikila” mfundo younikila pa Mat. 4:23 nwtsty)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mat. 5:31-48
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Onani Makambilano a Citsanzo.
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Nkhani: (6 min. olo kucepelapo) w16.03 mape. 31-32—Mutu: Pamene Satana Anali Kuyesa Yesu, Kodi Anam’tengela ku Kacisi Weni-weni, Kapena Anangomuonetsa Kacisiyo M’masomphenya Cabe?
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Odala ndi Anthu Amene Akuzunzidwa Cifukwa ca Cilungamo: (9 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Banja la M’bale Namgung: Linamangiwa Cifukwa ca Cikhulupililo, ndiyeno kambilanani zimene mwaphunzilapo (pitani pa mavidiyo ZOCITIKA NA KUFUNSA MAFUNSO).
“Pita Ukayanjane ndi m’Bale Wako Coyamba—Motani?”: (6 min.) Kukambilana. Kambilanani cifukwa cake kucita zili pa kadoti kothela ndiye kungakhale kofunika.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 3
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 141 na Pemphelo