February 1-7
LEVITIKO 26–27
Nyimbo 89 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1.)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Zimene Tingacite Kuti Tilandile Madalitso a Yehova”: (Mph. 10.)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 10.)
Lev. 26:16—Kodi Yehova analanga Aisiraeli na mlili m’lingalilo lotani? (it-2 617)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4.) Lev. 26:18-33 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3.) Yambani na makambilano acitsanzo. Gaŵilani kakhadi kongenela pa webusaiti yathu. (th phunzilo 11)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4.) Yambani na makambilano acitsanzo. Gaŵilani cofalitsa ca mu Thuboksi yathu. (th phunzilo 6)
Nkhani: (Mph. 5.) w09 8/1 30—Mutu: Kodi Mulungu Amafuna Kuti Nizipeleka Ndalama Zingati? (th phunzilo 16)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Sankhani Kutumikila Yehova”: (Mph. 15.) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Zimene Mungacite Kuti Muyenelele Ubatizo.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30.) lfb phunzilo 18, 19
Mawu Othela (Mph. 3.)
Nyimbo 2 na Pemphelo