February 8-14
NUMERI 1-2
Nyimbo 123 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1.)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Alinganiza Anthu Ake Mwadongosolo”: (Mph. 10.)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 10.)
Num. 1:2, 3—N’cifukwa ciani Aisiraeli anali kulembedwa m’kaundula? (it-2 764)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4.) Num. 1:1-19 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3.) Yambani na makambilano acitsanzo. Pemphani mwininyumba kuti muziphunzila naye Baibo. Ndiyeno, chulani na kukambilana vidiyo yakuti Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji? (koma musaitambitse). (th phunzilo 9)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4.) Yambani na makambilano acitsanzo. Sinthankoni ulaliki wanu kuti ugwilizane na nkhawa za mwininyumba, kenako ŵelengani lemba loyenelela. (th phunzilo 12)
Nkhani: (Mph. 5.) w08 7/1 21—Mutu: N’cifukwa Ciani Nthawi Zambili Baibo Imangochula Mafuko 12 a Isiraeli Pamene M’ceni-ceni Anali Mafuko 13? (th phunzilo 7)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Gulu Limene Limalalikila Aliyense”: (Mph. 10.) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Khala Bwenzi la Yehova—Kulalikila m’Citundu Cina. Kambilanani na omvetsela mbali zina za pa JW Language® app.
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 5.)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30.) lfb phunzilo 20, 21
Mawu Othela (Mph. 3.)
Nyimbo 148 na Pemphelo