January 25-31
LEVITIKO 24-25
Nyimbo 144 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1.)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Caka ca Ufulu Komanso Ufulu Wam’tsogolo”: (Mph. 10.)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 10.)
Lev. 24:20—Kodi mawu a Mulungu amalimbikitsa kubwezela? (w09 9/1 22 ¶4)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4.) Lev. 24:1-23 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba (Mph. 3.) Mukayamba makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki, koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 16)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4.) Yambani na makambilano acitsanzo. Gaŵilani mwininyumba kapepa koitanila kumisonkhano. Ndiyeno chulani na kukambilana vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? (koma musaitambitse) (th phunzilo 11)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5.) fg phunzilo 12 ¶6-7 (th phunzilo 14)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo (Mph. 5.)
“Tidzapeza Ufulu M’tsogolo mwa Thandizo la Mulungu na Khristu”: (Mph. 10.) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Pamene Mphepo ya Mkuntho Ikuyandikila, Pitilizani Kuyang’anitsitsa Yesu!—Madalitso a Ufumu a Mtsogolo.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30.) lfb phunzilo 17
Mawu Othela (Mph. 3.)
Nyimbo 12 na Pemphelo