January 4-10
LEVITIKO 18–19
Nyimbo 122 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1.)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Khalanibe na Khalidwe Loyela”: (Mph. 10.)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu (Mph. 10.)
Lev. 19:9, 10—Kodi Cilamulo cinaonetsa bwanji kuti Mulungu amaganizila osauka? (w06 6/15 22 ¶11)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4.) Lev. 18:1-15 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (Mph. 5.) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Pemphelo—Sal. 65:2. Nthawi iliyonse vidiyo ikaima, na imwe iimitseni na kufunsa omvetsela mafunso amene aonekela pasikilini.
Ulendo Woyamba: (Mph. 3.) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 3)
Nkhani: (Mph. 5.) w02 2/1 29—Mutu: Kodi Malamulo Oletsa Ukwati wa Pacibale Amene ali M’Cilamulo ca Mose Amagwila Nchito kwa Akhristu Lelolino Pamlingo Wotani? (th phunzilo 7)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Khala Bwenzi la Yehova—Tetezani Ana Anu: (Mph. 5.) Nkhani yokambidwa na mkulu. Onetsani vidiyoyi. Ndiyeno fotokozani zimene tiphunzilapo.—Miy. 22:3.
“Makolo, Phunzitsani Ana Anu Zimene Afunika Kudziŵa”: (Mph. 10.) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Mangani Nyumba Imene Idzakhalitsa—Tetezani Ana Anu ku “Zinthu Zoipa”.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30.) lfb phunzilo 13
Mawu Othela (Mph. 3.)
Nyimbo 113 na Pemphelo