February 14-20
1 SAMUELI 3-5
Nyimbo 1 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Ni Mulungu Woganizila Ena”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
1 Sam. 3:3—Tidziŵa bwanji kuti Samueli sanali kugona m’Malo Oyela Koposa? (w05 3/15 21 ¶6)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Sam. 3:1-18 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Yambani na makambilano acitsanzo. Pemphani mwininyumba kuti muziphunzila naye Baibo m’kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya. (th phunzilo 11)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Gaŵilani kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! na kuyambitsa phunzilo la Baibo m’phunzilo 01. (th phunzilo 15)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lffi phunzilo 03 mfundo 6 (th phunzilo 14)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Zimene Tingaphunzile kwa Samueli”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Zimene Tingaphunzile Kwa Iwo—Samueli.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 77
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 64 na Pemphelo