Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

February 13-19

1 MBIRI 13-16

February 13-19

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Kutsatila Malangizo Kumacititsa Kuti Zinthu Zitiyendele Bwino”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 1 Mbiri 16:31—N’cifukwa ciyani Alevi anaimba kuti, “Yehova wakhala mfumu”? w14 1/15 10 ¶14)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Mbiri 13:1-14 (th phunzilo 11)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mukayamba, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 18)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni cofalitsa ca m’Thuboksi yathu. (th phunzilo 7)

  • Nkhani: (Mph. 5) w16.01 13-14 ¶7-10—Mutu: “Cikondi Cimene Khristu Ali Naco Cimatikakamiza.”—2 Akor. 5:14. (th phunzilo 8)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 86

  • Khala Bwenzi la Yehova—Uzimvetsela Mwachelu pa Misonkhano: (Mph. 5) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi. Ndiyeno ngati n’kotheka funsani mafunso ana amene munawasankhilatu. Afunseni kuti: N’cifukwa ciyani tiyenela kumvetsela mwachelu pa misonkhano? N’ciyani cingakuthandize kucita zimenezi?

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 10)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 37 mfundo 6 cidule cake, kubweleza, na colinga

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 21 na Pemphelo