February 27–March 5
1 MBIRI 20-22
Nyimbo 133 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Thandizani Acinyamata Kuti Apambane”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
1 Mbiri 21:15—Kodi vesiyi itiphunzitsa ciyani za Yehova (w05 10/1 11 ¶6)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Mbiri 20:1-8 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mukayamba, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 1)
Ulendo wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni kapepala komuitanila ku msonkhano ndipo chulani na kukambilanako vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? (Koma musaitambitse.) (th phunzilo 19)
Nkhani: (Mph. 5) w16.03 10-11 ¶10-15—Mutu: Acinyamata—Pitani Patsogolo Kuti Mukabatizike. (th phunzilo 16)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Seŵenzetsani Mfundo za m’Baibo Pothandiza Ana Anu Kuti Apambane”: (Mph. 10) Kukambilana komanso kutamba vidiyo.
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 5)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 38 mfundo 5 komanso cidule cake, kubweleza, na colinga
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 5 na Pemphelo