February 6-12
1 MBIRI 10-12
Nyimbo 94 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kulitsani Cikhumbo Canu Cofuna Kucita Cifunilo ca Mulungu”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
1 Mbiri 12:33—Ni citsanzo cabwino citi cimene amuna 50,000 a fuko la Zebuloni anapeleka? it-1 1058 ¶5-6)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Mbiri 11:26-47 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Kenako m’pempheni kuti muyambe kuphunzila naye Baibo. (th phunzilo 12)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Chulani na kukambilanako vidiyo yakuti Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji? (Koma musaitambitse.) (th phunzilo 6)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 09 mawu oyamba na mfundo 1-3 (th phunzilo 18)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Fufuzani Kuti Mudziŵe Maganizo a Mulungu”: (Mph. 10) Kukambilana na kutamba vidiyo.
“Dziikileni Zolinga za pa Nyengo ya Cikumbutso”: (Mph. 5) Kukambilana.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 37 mfundo 1-5
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 91 na Pemphelo