January 16-22
1 MBIRI 1-3
Nyimbo 96 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Baibo—Buku Limene Limakamba Zenizeni Osati Nthano”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
1 Mbiri 3:1-3—N’cifukwa ciyani nthawi zina maina a akazi anali kulembedwa m’kaundula wa mibadwo? (it-1 911 ¶3-4)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Mbiri 1:43-54 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Gaŵilani magazini yofotokoza nkhani imene mwininyumbayo wayambitsa. (th phunzilo 4)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Gaŵilani cofalitsa ca m’Thuboksi yathu. (th phunzilo 1)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 08 mfundo 7, komanso mbali yakuti Anthu Ena Amakamba Kuti (th phunzilo 8)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Limbitsani Cikhulupililo Canu pa Mawu a Mulungu”: (Mph. 15) Kukambilana na kutamba vidiyo.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 34
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 89 na Pemphelo