January 23-29
1 MBIRI 4-6
Nyimbo 42 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Mapemphelo Anga Amavumbula Ciyani za Ine?”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
1 Mbiri 5:10—Kodi kugonjetsedwa kwa Ahagara kungatilimbikitse bwanji pamene tikukumana na mavuto aakulu mu umoyo wathu? (w05 10/1 9 ¶7)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Mbiri 6:61-81 (th phunzilo 2)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mukayamba, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 3)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitanzo. Chulani na kukambilanako vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (Koma musaitambitse.) (th phunzilo 14)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 8 cidule cake, kubweleza, komanso colinga (th phunzilo 9)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Konzekelani Palipano Musanadwale Mwadzidzidzi Kapena Kukumana na Ngozi”: (Mph. 15) Kukambilana na kutamba vidiyo. Nkhaniyi ipatsidwe kwa mkulu. Patsani omvela nthawi kuti akambepo zimene aphunzila mu vidiyo.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 35
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 88 na Pemphelo