January 30–February 5
1 MBIRI 7-9
Nyimbo 84 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Na Thandizo la Yehova, Mungakwanitse Kucita Utumiki Wovuta”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
1 Mbiri 9:33—Kodi vesiyi itithandiza bwanji kumvetsa kuti kuimba nyimbo n’kofunika kwambili pa kulambila kwathu? (w10 12/15 21 ¶6)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Mbiri 7:1-13 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Musiyileni kakhadi koloŵela pa jw.org. (th phunzilo 16)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni cofalitsa ca m’Thuboksi yathu. (th phunzilo 20)
Nkhani: (Mph. 5) w21.06 3-4 ¶3-8—Mutu: Thandizani Maphunzilo Anu a Baibo Kuseŵenzetsa Zimene Amaphunzila. (th phunzilo 13)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Yehova Amatithandiza Kupilila Mayeso”: (Mph. 15) Kukambilana na kutamba vidiyo.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 36
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 31 na Pemphelo