January 9-15
2 MAFUMU 24-25
Nyimbo 60 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Khalanibe Maso”:(Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
2 Maf. 24:3, 4—Kodi mavesi awa atiphunzitsa ciyani za Yehova? (w05 8/1 12 ¶1)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Maf. 24:1-17 (th phunzilo 11)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Wobwelelako: Pemphelo—1 Yoh. 5:14. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvela mafunso amene aonekela.
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. (th phunzilo 15)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo, ndipo yambitsani phunzilo la Baibo m’phunzilo 01 la bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! (th phunzilo 19)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 15)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff kubweleza cigawo 2
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 54 na Pemphelo