Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

January 13-19

MASALIMO 135-137

January 13-19

Nyimbo 2 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. “Ambuye Wathu Ndi Wamkulu Kuposa Milungu Ina Yonse”

(Mph. 10)

Yehova waonetsa kuti ali na mphamvu zolamulila cilengedwe conse (Sal. 135:​5, 6; it-2-E 661 ¶4-5)

Iye amateteza anthu ake (Eks. 14:​29-31; Sal. 135:14)

Amatithandiza tikafooka (Sal. 136:23; w21.11 6 ¶16)

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Sal. 135:​1, 5​—N’cifukwa ciyani mawu akuti “Ya” amaseŵenzetsedwa kaŵili-kaŵili m’Baibo? (it-1-E 1248)

  • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?

3. Kuŵelenga Baibo

(Mph. 4) Sal. 135:​1-21 (th phunzilo 11)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Kuyambitsa Makambilano

(Mph. 3) ULALIKI WAMWAYI. Patsanani mafoni namba na munthu amene waonetsa cidwi. (lmd phunzilo 2 mfundo 4)

5. Kubwelelako

(Mph. 4) KU NYUMBA NA NYUMBA. Muitanileni ku misonkhano. (lmd phunzilo 9 mfundo 4)

6. Kufotokoza Zimene Mumakhulupilila

(Mph. 5) Citsanzo. ijwfq nkhani 7​—Mutu: Kodi Mboni za Yehova ni Akhristu? (th phunzilo 12)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 10

7. Zofunikila za Mpingo

(Mph. 15)

8. Phunzilo la Baibo la Mpingo

Mawu Othela (Mph. 3) | Nyimbo 90 na Pemphelo