Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

February 17-23

MIYAMBO 1

February 17-23

Nyimbo 88 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mwana wa Solomo akumvetsela malangizo acikondi a bambo ake

1. Inu Acinyamata, Kodi Mudzamvela Ndani?

(Mph. 10)

[Tambitsani VIDIYO YAKUTI Mfundo zokhudza buku la Miyambo.]

Khalani anzelu ndipo muzimvela makolo anu (Miy. 1:8; w17.11 29 ¶16-17; onani pacikuto)

Musamamvele anthu amene amacita zoipa (Miy. 1:​10, 15; w05 2/15 19-20 ¶11-12)

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Miy. 1:22​—Kodi m’Baibo, mawu lakuti “wopusa” komanso akuti “kupusa” amatanthauza ciyani nthawi zambili? (it-1-E 846)

  • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?

3. Kuŵelenga Baibo

(Mph. 4) Miy. 1:​1-23 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Kuyambitsa Makambilano

(Mph. 2) ULALIKI WAPOYELA. Munthu akufuna kukangana nanu. (lmd phunzilo 6 mfundo 5)

5. Kuyambitsa Makambilano

(Mph. 2) ULALIKI WAPOYELA. Patsanani mafoni namba na munthu amene waonetsa cidwi. (lmd phunzilo 1 mfundo 5)

6. Kubwelelako

(Mph. 2) ULALIKI WAMWAYI. Uzani munthu za pulogilamu yathu yophunzitsa Baibo, ndipo m’patseni kakhadi kopemphela phunzilo la Baibo. (lmd phunzilo 9 mfundo 5)

7. Kupanga Ophunzila

(Mph. 5) lff phunzilo 16 mfundo 6. Seŵenzetsani nkhani yopezeka pa mbali yakuti “Fufuzani” kuti muthandize wophunzila amene amakayikila ngati zozizwitsa za Yesu zinacitikadi. (th phunzilo 3)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 89

8. Zofunikila za Mpingo

(Mph. 15)

9. Phunzilo la Baibo la Mpingo

(Mph. 30) bt mutu 22 ¶15-21

Mawu Othela (Mph. 3) | Nyimbo 80 na Pemphelo