UMOYO NA UTUMIKI WATHU–KABUKU KA MISONKHANO July 2016
Maulaliki a Citsanzo
Maulaliki a citsanzo ogaŵila Nsanja ya Mlonda ndi kabuku ka Uthenga Wabwino Wocokela kwa Mulungu. Seŵenzetsani maulaliki a citsanzo pokonza ulaliki wanu.
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Tamandani Yehova Womvela Pemphelo
N’cifukwa ciani tiyenela kumachula m’mapemphelo athu zimene talonjeza Yehova? (Masalimo 61-
UMOYO WATHU WACIKHIRISTU
Kukhala na Umoyo Wosafuna Zambili Kudzatithandiza Kutamanda Mulungu
Kodi kukhala na umoyo wosafuna zambili kudzakuthandizani kucita ciani? Mungatengele bwanji citsanzo ca Yesu ca kukhala na umoyo wosafuna zambili?
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Anthu a Yehova ni Okangalika pa Kulambila Koona
Kodi cangu ca Davide cingatiphunzitse ciani? Kodi kukangalika kumatithandiza kucita ciani? (Masalimo 69–
UMOYO WATHU WACIKHIRISTU
Kodi Mungayeseko kwa Caka Cimodzi?
Anthu amene amacitako upainiya amakhala ndi umoyo wokhutilitsa ndipo amapeza madalitso ambili.
UMOYO WATHU WACIKHIRISTU
Ndandanda ya Upainiya wa Nthawi Zonse
Mungadabwe kuti ngakhale amene ali ndi zolepheletsa angathe kucita upainiya.
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Muzikumbukila Nchito za Yehova
Kodi nchito za Yehova ziphatikizapo ciani? Kodi kuganizila nchito za Yehova kungatithandize bwanji? (Psalms 74-
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Kodi Munthu Wofunika Kwambili pa Umoyo Wanu N’ndani?
Wolemba Masalimo 83 anaonetsa kuti Yehova ndiye munthu wofunika kwambili pa umoyo wake. Kodi na ife tingaonetse bwanji kuti Yehova ndiye munthu wofunika kwambili pa umoyo wathu?