July 11- 17
MASALIMO 69–73
Nyimbo 92 na Pemphelo
Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Anthu a Yehova ni Odzipeleka pa Kulambila Koona”: (Mph. 10)
Sal. 69:9—Kudzipeleka kwathu pa kulambila koona kuyenela kuonekela (w10 12/15-CN, masa. 7-11 ndime 2-17)
Sal. 71:17, 18—Acikulile angathandize acicepele kukhala odzipeleka (w14 1/1 , masa. 23-25 ndime 4-10)
Sal. 72:3, 12, 14, 16-19—Kudzipeleka kwathu kumatisonkhezela kuuzako ena zimene Ufumu wa Mulungu udzacitila anthu (w15 10/1 16 ndime 3; w10 8/15-CN, tsa. 32 ndime 19-20)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)
Sal. 69:4, 21—Kodi mavesi amenewa anakwanilitsika bwanji pa Mesiya? (w11 8/15-CN, tsa. 11 ndime 17; w11 8/15-CN, tsa. 15 ndime 15)
Sal. 73:24—Kodi Yehova amatsogolela bwanji anthu ake ku ulemelelo? (w13 2/15-CN, masa. 25-26 ndime 3-4)
Kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?
Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ningaseŵenzetse mu ulaliki?
Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Sal. 73:1-28
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) Nsanja ya Mlonda ya 2016 Na. 4 nkhani ya pacikuto—Yalani maziko a ulendo wobwelelako.
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Nsanja ya Mlonda ya 2016 Na. 4 nkhani ya pacikuto
Phunzilo la Baibulo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) Uthenga Wabwino phunzilo 5 ndime 3-4
UMOYO WATHU WACIKHIRISTU
“Kodi Mungayeseko kwa Caka Cimodzi?”: (Mph. 15) Mwacidule, kambilanani nkhani imeneyi. Mukambilanenso “Ndandanda ya Upainiya wa Nthawi Zonse.” Onetsani ndi kukambilana vidiyo ya pa JW Broadcasting yakuti Khalani na Colinga Cimene Cidzakupindulitsani Kwamuyaya. (Pitani pa VIDEO ON DEMAND > TEENAGERS.)
Phunzilo la Baibulo la Mpingo: (Mph. 30) ia mutu 19 ndime 17-31, bokosi pa tsa. 170, ndi kubwelelamo pa tsa. 171
Kubwelelamo ndi Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)
Nyimbo 123 na Pemphelo