MASALIMO 69-73
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU |Anthu a Yehova ni Okangalika pa Kulambila Koona
Cangu cathu pa kulambila koona cizionekela
69:9
-
Davide anali wacangu potumikila Yehova umoyo wake wonse
-
Davide sanalole munthu aliyense kutsutsana ndi Yehova kapena kutonza dzina la Mulungu
Acikulile angathandize acicepele kukhala okangalika
71:17, 18
-
Wolemba salimo imeneyi amene mwina ndi Davide, anaonetsa kuti anali wofunitsitsa kulimbikitsa mbadwo wotsatila
-
Makolo ndi Akhiristu ofikapo mwauzimu angaphunzitse acicepele
Tikakhala acangu timauzako ena zimene Ufumu wa Mulungu udzacitila anthu
72:3, 12, 14, 16-19
-
Vesi 3—Anthu onse adzakhala pa mtendele
-
Vesi 12—Osauka adzalanditsidwa
-
Vesi 14—Ciwawa cidzatha
-
Vesi 16—Aliyense adzakhala ndi cakudya ca mwana alilenji