UMOYO WATHU WACIKHIRISTU
Ndandanda ya Upainiya wa Nthawi Zonse
Upainiya wa nthawi zonse umafuna ndandanda yabwino. Ngati mumalalikila kwa maola 18 mlungu uliwonse, mukhoza kucita upainiya ndipo mungakhale ndi nthawi yocita zinthu zina. Ndandanda yotele, idzakuthandizani kukhala ndi nthawi yosamalila zakugwa mwadzidzidzi, monga matenda kapena nyengo ngati sili bwino. Pa chati cimene cili munsimu pali ndandanda zimene zingathandize amene amagwila nchito ya maola ocepa, amene amagwila nchito ya tsiku lonse, kapena amene ali ndi thanzi lofooka. Mukasintha zocita zina, wina m’banja angayambe kucita upainiya mu September. Bwanji osakambilana zimenezi pa kulambila kwanu kwa pa banja mlungu wotsatila?
Mande |
NCHITO |
Ciŵili |
NCHITO |
Citatu |
NCHITO |
Cinayi |
Maola 6 |
Cisanu |
Maola 6 |
Ciŵelu |
Maola 4 |
Sondo |
Maola 2 |
Mande |
Maola 2 |
Ciŵili |
Maola 2 |
Citatu |
MISONKHANO YA MKATI MWA MLUNGU |
Cinayi |
Maola 2 |
Cisanu |
Maola 2 |
Ciŵelu |
Maola 6 |
Sondo |
Maola 4 |
Mande |
KUPUMULA |
Ciŵili |
Maola 3 |
Citatu |
Maola 3 |
Cinayi |
Maola 3 |
Cisanu |
Maola 3 |
Ciŵelu |
Maola 3 |
Sondo |
Maola 3 |