July 18- 24
MASALIMO 74-78
Nyimbo 110 ndi Pemphelo
Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Muziganizila Nchito za Yehova”: (Mph. 10)
Sal. 74:16; 77:6, 11, 12—Muziganizila mozama nchito za Yehova (w15 8/15, tsa. 10 ndime 3-4; w04 3/1-CN, masa. 19-20; w03 7/1-CN, tsa. 10 ndime 6-7)
Sal. 75:4-7—Nchito za Yehova ziphatikizapo kusankha amuna odzicepetsa kuti azisamalila mpingo (w06 7/15 -CN, tsa. 11 ndime 2; it-E 1, tsa. 1160 ndime 7)
Sal. 78:11-17—Ganizilani mmene Yehova anathandizila anthu ake (w04 4/1-CN, masa. 21-22)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)
Sal. 78:2—Kodi mau a vesi imeneyi anakwanilitsika bwanji pa Mesiya? (w11 8/15-CN, tsa. 11 ndime 14)
Sal. 78:40, 41—Malinga ni mavesi aya, kodi zocita zathu zingakhudze bwanji Yehova? (w12-CN 11/1, tsa. 14 ndime 5; w11-CN 7/1, tsa. 10)
Kodi kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?
Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ningaseŵenzetse mu ulaliki?
Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Sal. 78:1-21
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) Nsanja ya Mlonda yogaŵila ya 2016 Na. 4 tsa. 16—Chulani za copeleka.
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Nsanja ya Mlonda yogaŵila ya 2016 Na. 4
Phunzilo la Baibulo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) Uthenga Wabwino phunzilo 5 ndime 6-7
UMOYO WATHU WACIKHIRISTU
Zosoŵa za pa mpingo: (Mph. 10)
“Yehova Analenga Zinthu Zonse”: (Mph. 5)Kukambilana. Tambitsani vidiyo ya pa jw.org yakuti Yehova Analenga Zinthu Zonse”. (Pitani pa MABUKU > MAVIDIYO.) Pambuyo pake, pemphani ana amene asankhidwa kuti abwele kutsogolo. Ndiyeno, afunseni mafunso ogwilizana ndi vidiyo imeneyo.
Phunzilo la Baibulo la Mpingo: (Mph. 30) ia mutu. 20 ndime 1-13
Kubwelelamo ndi Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)
Nyimbo 73 ndi Pemphelo