UMOYO NA UTUMIKI WATHU–KABUKU KA MISONKHANO July 2018
Makambilano Acitsanzo
Makambilano otsatizana-tsatizana a mmene mfundo za m’Baibo zimathandizila mabanja kukhala acimwemwe.
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Tizipimila Ena Mowolowa Manja
Munthu wowolowa manja amathandiza ena mokondwela na kuwalimbikitsa.
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Khala Wotsatila Wanga—Motani?
Kodi tifunika kusumika maganizo athu pa ciani ngati tayamba kuganizila zinthu zakale zimene zingaticenjeneke?
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Fanizo la Msamariya Wacifundo
Otsatila a Yesu afunika kuyesetsa kukonda anthu, ngakhale amene aoneka kuti ni osiyana nawo kwambili.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
N’cifukwa Ciani Kusatengako Mbali Mundale N’kofunika? (Mika 4:2)
Potengela Mulungu wathu wopanda tsankho, tifunika kucitila anthu onse zabwino.
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Ndinu Ofunika Kwambili Kuposa Mpheta Zambili”
Tingatengele bwanji citsanzo ca Yehova pankhani yodela nkhawa anthu amene akuzunzidwa?
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Fanizo la Mwana Woloŵelela
Kodi fanizo ili litiphunzitsa ciani pa nkhani ya kukhala wozindikila, kudzicepetsa, na kudalila Yehova Mulungu?