Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

July 16-22

LUKA 10-11

July 16-22
  • Nyimbo 100 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Fanizo la Msamariya Wacifundo”: (10 min.)

    • Luka 10:29-32—Wansembe, kenako Mlevi, analephela kuthandiza Myuda mnzawo amene anavulazidwa ndi acifwamba [Tambitsani kavidiyo “Mseu Wocoka ku Yerusalemu Kupita ku Yeriko” ka pa Luka 10:30, nwtsty zithunzi.] (w02 9/1 mape. 16-17 mapa. 14-15)

    • Luka 10:33-35—Msamariya anaonetsa cikondi capadela kwa munthu wovulazidwayo (“Msamariya wina” “kumanga mabala ake, [kuthila] mafuta ndi vinyo m’mabalamo” , “Kunyumba ya alendonwtsty mfundo zounikila pa Luka 10:33, 34)

    • Luka 10:36, 37—Tiyenela kukonda munthu aliyense, osati cabe anthu amene timafanana nawo mtundu, cikhalidwe, dziko, kapena olemela olo osauka anzathu (w98 7/1 peji 31 pala. 2)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Luka 10:18—Kodi Yesu anatanthauzanji pouza ophunzila ake 70 kuti: “Ndinayamba kuona Satana atagwa kale ngati mphezi kucokela kumwamba”? (“Ndinayamba kuona Satana atagwa kale ngati mphezi kucokela kumwambanwtsty mfundo zounikila; w08 3/15 peji 31 pala. 12)

    • Luka 11:5-9—Kodi fanizo la munthu wokakamila [wolimbikila] litiphunzitsa ciani za pemphelo? (“Bwanawe, ndibwelekeko mitanda itatu ya mkate”, “Usandivutitse ine”, “kukakamilanwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Luka 10:1-16

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Mwininyumba akambe zimene anthu a m’gawo lanu amakamba posafuna kulalikidwa.

  • Kubwelelako Koyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Munthu akukuuzani kuti ali kudya.

  • Vidiyo ya Kubwelelako Kaciŵili: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 24

  • N’cifukwa Ciani Kusatengako Mbali Mundale N’kofunika? (Mika 4:2)”: (15 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi .

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 29

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 146 na Pemphelo