Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

July 23-29

LUKA 12-13

July 23-29
  • Nyimbo 4 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Ndinu Ofunika Kwambili Kuposa Mpheta Zambili”: (10 min.)

    • Luka 12:6—Ngakhale mbalame zing’ono-zing’ono Mulungu saziiŵala (“mphetanwtsty mfundo younikila)

    • Luka 12:7—Yehova amatidziŵa bwino kwambili. Uwu ni umboni wakuti amatikonda ngako (“ngakhale tsitsi lonse la m’mutu mwanu analiŵelenganwtsty mfundo younikila)

    • Luka 12:7—Yehova amaona aliyense wa ise kukhala wofunika (cl peji 241 mapa. 4-5)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Luka 13:24—Kodi zimene Yesu anakamba pa lembali zitanthauza ciani? (“Yesetsani mwamphamvunwtsty mfundo younikila)

    • Luka 13:33—N’cifukwa ciani Yesu anakamba mau amenewa? (“n’kosayenelanwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Luka 12:22-40

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Kubwelelako Kaciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno itanilani mwininyumba ku misonkhano.

  • Kubwelelako Kacitatu: (3 min. olo kucepelapo) Sankhani mwekha lemba, ndipo gaŵilani cofalitsa cophunzitsila Baibo.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) lv mape. 184-185 mapa. 4-5

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 116

  • Sayenda Koma Sanaiŵalidwe: (15 min.) Tambitsani vidiyoyi. Pambuyo pake, kambilanani mafunso aya:

    • Kodi ofalitsa atatuwa anakumana na mavuto anji?

    • Kodi Yehova anawaonetsa bwanji kuti sanawaiŵale?

    • Kodi ofalitsawo anapitiliza bwanji kutumikila Yehova ngakhale kuti anakumana na mavuto? Nanga kucita zimenezi kunawalimbikitsa bwanji ofalitsa ena?

    • Kodi okalamba kapena odwala amene ali mu mpingo wanu mungawaonetse bwanji cikondi?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy Mutu 30

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 5 na Pemphelo