July 9-15
LUKA 8-9
Nyimbo 13 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Khala Wotsatila Wanga—Motani?”: (10 min.)
Luka 9:57, 58—Amene amatsatila Yesu afunika kudalila Yehova (it-2 peji 494)
Luka 9:59, 60—Amene amatsatila Yesu amaika Ufumu wa Mulungu patsogolo mu umoyo wawo (“kukaika malilo a bambo anga,” “Aleke akufa aike akufa awo” nwtsty mfundo younikila)
Luka 9:61, 62—Amene amatsatila Yesu salola zinthu za dziko kuwacenjeneka (“Kugaula” nwtsty zithunzi; w12 4/15 mape. 15-16 mapa. 11-13)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Luka 8:3—Kodi Akhristu amenewa anali “kutumikila” Yesu na atumwi m’njila yanji? (“anali kutumikila Yesu ndi atumwiwo” nwtsty mfundo younikila)
Luka 9:49, 50—N’cifukwa ciani Yesu sanaletse munthu wina kutulutsa ziwanda, olo kuti sanali wotsatila wake? (w08 3/15 peji 31 pala. 3)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Luka 8:1-15
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.
Vidiyo ya Kubwelelako Koyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Nkhani: (6 min. olo kucepelapo) w12 3/15 mape. 27-28 mapa. 11-15—Mutu: Kodi Tiyenela Kudandaula pa Zimene Tinasiya Pocilikiza Ufumu?
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (15 min.)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 28, na bokosi pa peji 70
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 110 na Pemphelo