August 2-8
DEUTERONOMO 22–23
Nyimbo 1 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amadela Nkhawa Nyama”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Deut. 23:19, 20—N’cifukwa ciani Aisiraeli anali kuloledwa kulipilitsa mlendo ciwongoladzanja koma osati Mwisiraeli mnzawo? (it-1 600)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Deut. 23:1-14 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
“Wonjezelani Cimwemwe Canu mu Ulaliki—Afikeni Pamtima Anthu”: (Mph. 9) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Pezani Cimwemwe pa Nchito Yopanga Ophunzila—Nolani Maluso Anu—Kuwafika Pamtima Anthu.
Nkhani: (Mph. 5) g 4/15 13—Mutu: Kodi Kupha Nyama N’kulakwa? (th phunzilo 14)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 15)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 49
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 121 na Pemphelo