August 23-29
DEUTERONOMO 29-30
Nyimbo 3 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kutumikila Yehova Sikovuta”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Deut. 29:4—N’cifukwa ciani Aisiraeli ni citsanzo coticenjeza? (it-1 665 ¶3)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Deut. 29:1-18 (th phunzilo 2)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Yambani na makambilano acitsanzo. Gaŵilani kakhadi kongenela pa webusaiti yathu. (th phunzilo 1)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Pemphani mwininyumba kuti muziphunzila naye Baibo, ndiyeno chulani za vidiyo yakuti Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji? (koma musaitambitse) (th phunzilo 6)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lvs 226-227 ¶3-5 (th phunzilo 13)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Kukhala Wolimba Mtima Sikovuta” (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti, Tengelani Citsanzo ca Anthu Olimba Mtima, Osati Amantha!
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 52
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 7 na Pemphelo