July 12-18
DEUTERONOMO 13–15
Nyimbo 38 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amadela Nkhawa Osauka”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Deut. 14:21—Kodi tingaphunzilepo ciani pa lamulo loletsa kuŵilitsa mwana wa mbuzi mu mkaka wa make? (w06 4/1 31)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Deut. 13:1-18 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Wobwelelako: Kuvutika—1 Yoh. 5:19. Nthawi iliyonse vidiyo ikaima, na imwe iimitseni na kufunsa omvetsela mafunso amene aonekela pasikilini.
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 6)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Yambani na makambilano acitsanzo. Gaŵilani cofalitsa ca m’Thuboksi yathu. (th phunzilo 11)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Musamade Nkhawa”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Cikondi Sicitha Olo Kuti . . . Ndimwe Osauka—Congo.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 45
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 31 na Pemphelo