July 26–August 1
DEUTERONOMO 19–21
Nyimbo 141 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Moyo wa Munthu Ni Wamtengo Wapatali Kwa Yehova”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Deut. 21:19—N’cifukwa ciani bwalo loweluzila milandu linali kukhala pa cipata ca mzinda? (it-1 518 ¶1)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Deut. 19:1-14 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Mukayamba na makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso, loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 12)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Chulani za vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (koma musaitambitse) (th phunzilo 6)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) bhs 138 ¶8 (th phunzilo 13)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Yenda pa Njila Yako Popanda Cokuopseza”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Pambuyo pake, funsani mafunso awa: N’cifukwa ciani tiyenela kuyesetsa kupewa Ngozi? Ni zinthu ziti zimene tingacite kuti tipewe ngozi?
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 48
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 117 na Pemphelo