Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

UMOYO WATHU WACIKHRISTU | DZIIKILENI ZOLINGA ZA CAKA CA UTUMIKI CATSOPANO

Funsilani Kuloŵa Sukulu ya Alengezi a Ufumu

Funsilani Kuloŵa Sukulu ya Alengezi a Ufumu

Kuti mufunsile kukaloŵa Sukulu ya Alengezi a Ufumu (SKE), musacite kuyembekezela mpaka zinthu zikakhale bwino kwambili pa umoyo wanu. Cofunikila kwenikweni ni kukhala munthu wauzimu, komanso wofunitsitsa kulandila utumiki uliwonse umene mungapatsidwe m’gulu la Yehova.—Yes. 6:8.

ONELELANI VIDIYO YAKUTI LOŴANI PA KHOMO LA ZOCITA ZAMBILI M’CIKHULUPILILO—FUNSILANI KULOŴA SUKULU YA ALENGEZI A UFUMU, KENAKO YANKHANI MAFUNSO AWA:

  • N’cifukwa ciyani Gabriel anali kukayikila zofunsila kuti akaloŵe Sukulu ya Alengezi a Ufumu? Nanga analimbikitsidwa bwanji atasinkhasinkha mfundo ya pa Afilipi 4:13?