August 22-28
1 MAFUMU 7
Nyimbo 7 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Zimene Tingaphunzilepo pa Zipilala Ziŵili”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
1 Maf. 7:23—Kodi “thanki yamkuwa” yaikulu imene inamangidwa pa kacisi itiphunzitsa ciyani? (it-1 263)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Maf. 7:1-12 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mukayamba kukambilana, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 6)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Ndipo m’gaŵileni kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! na kumuonetsa mmene phunzilo la Baibo limacitikila. (th phunzilo 3)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 06 mfundo 6, na mbali yakuti Anthu Ena Amakamba Kuti (th phunzilo 8)
UMOYO WATHU WACIKHRSITU
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 5)
“Kampeni Yapadela Yoyambitsa Maphunzilo a Baibo mu September”: (Mph. 10) Nkhani yokambilana yokambidwa na woyang’anila utumiki. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Phunzilo la Baibo—Sal. 37:29. Fotokozani makonzedwe amene mpingo wapanga okhudza kampeni imeneyi.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 17
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 13 na Pemphelo