July 11-17
2 SAMUELI 20-21
Nyimbo 62 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova ni Mulungu Wacilungamo”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
2 Sam. 21:15-17—Kodi tiphunzilapo zotani pa nkhani imeneyi? (w13 1/15 31 ¶14)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Sam. 20:1-13 (th phunzilo 2)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Wobwelelako: Colinga ca Mulungu—Yes. 55:11. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvela mafunso amene aonekela mu vidiyo.
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’fotokozeleni mmene phunzilo la Baibo limacitikila, na kum’patsa kakhadi kofunsila phunzilo la Baibo. (th phunzilo 4)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!, na kumuonetsa mmene phunzilo la Baibo limacitikila. (th phunzilo 11)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Dziikileni Zolinga za Caka ca Utumiki Catsopano—Katumikilen’koni Kumalo Osowa”: (Mph. 10) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Loŵani pa Khomo la Zocita Zambili m’Cikhulupililo—Katumikilenkoni Kumalo Osowa.
“Mmene Tingaseŵenzetsele Makambilano Acitsanzo”: (Mph. 5) Nkhani yokambidwa na woyang’anila Msonkhano wa Umoyo na Utumiki.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 12
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 3 na Pemphelo