Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova ni Mulungu Wacilungamo

Yehova ni Mulungu Wacilungamo

Yehova sanaiŵale zinthu zopanda cilungamo zimene Sauli na a m’banja lake anacita kwa Agibeoni (2 Sam. 21:1, 2)

Siliva na golide sakanakwanitsa kumasula Sauli na a m’banja lake ku mlandu wa magazi (Num. 35:31, 33; 2 Sam. 21:3, 4)

Mbadwa 7 za Sauli zinaphedwa kuti pakhale cilungamo (2 Sam. 21:5, 6; it-1 932 ¶1)

Kodi lemba la Aroma 12:19-21 lingatilimbikitse bwanji pamene ena aticita zinthu zopanda cilungamo?