Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CITANI KHAMA PA ULALIKI

Makambilano Acitsanzo

Makambilano Acitsanzo

Ulendo Woyamba

Funso: Tidziŵa bwanji kuti mavuto amene timakumana nawo si cilango cocokela kwa Mulungu?

Lemba: Yak. 1:13

Ulalo: N’cifukwa ciyani timavutika?

PEZANI LEMBALI M’CIDA ICI CA M’THUBOKSI YATHU:

Ulendo Wobwelelako

Funso: N’cifukwa ciyani timavutika?

Lemba: 1 Yoh. 5:19

Ulalo: Kodi Mulungu amamva bwanji akaona kuti tikuvutika?

PEZANI LEMBALI M’CIDA ICI CA M’THUBOKSI YATHU: