August 14-20
NEHEMIYA 8-9
Nyimbo 110 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Cimwemwe Cimene Yehova Amapeleka Ndico Malo Anu Acitetezo”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Neh. 8:2, 8—Ngati Aisiraeli anali kukwanitsa “kumvetsela ndi kuzindikila” zimene zinali kuŵelengedwa m’Cilamulo, n’cifukwa ciyani Alevi anali kucifotokozelanso cilamuloco? (it-1 145 ¶2)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Neh. 8:1-12 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni cofalitsa ca m’Thuboksi yathu. (th phunzilo 13)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muitanileni ku misonkhano. Ndiyeno chulani na kukambilanako vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? (Koma musaitambitse) (th phunzilo 11)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 11 mfundo 5 na mbali yakuti Anthu Ena Amakamba Kuti (th phunzilo 8)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Mungathandize Kuti m’Banja Lanu Mukhale Cimwemwe”: (Mph. 15) Kukambilana na kuonelela vidiyo.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 54
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 123 na Pemphelo