Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Ezara akuŵelengela anthu Cilamulo na kutamanda Yehova

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Cimwemwe Cimene Yehova Amapeleka Ndico Malo Anu Acitetezo”

“Cimwemwe Cimene Yehova Amapeleka Ndico Malo Anu Acitetezo”

Anthu anasonkhana kuti amvetsele pamene Ezara anali kuŵelenga Cilamulo (Neh. 8:1, 2; w13 10/1 19-20 ¶2; onani cithunzi pa cikuto)

Iyi inali nthawi yolambila Yehova mosangalala, osati yolila cifukwa cokumbukila macimo akale (Neh. 8:9, 11, 12)

Cimwemwe cimene Yehova amapeleka ni malo acitetezo kwa atumiki ake (Neh. 8:10; w07 7/15 22 ¶9-10)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Nili na zifukwa zotani zokhalila wacimwemwe ngakhale kuti nimakumana na mavuto?’