Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

August 21-27

NEHEMIYA 10-11

August 21-27

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Anadzimana Zinazake Cifukwa Comvela Yehova”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Neh. 10:34—N’cifukwa ciyani anthu anafunika kumapeleka nkhuni? (w06 2/1 11 ¶1)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Neh. 10:28-39 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU