Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Anadzimana Zinazake Cifukwa Comvela Yehova

Anadzimana Zinazake Cifukwa Comvela Yehova

Mabanja ena anapemphedwa kusiya nyumba na minda yawo kuti akakhale mumzinda wa Yerusalemu (Neh. 11:1; w98 10/15 22 ¶13)

Amene anadzipeleka kucita zimenezi anadalitsidwa (Neh. 11:2; w86 2/15 26)

Madalitso a Yehova nthawi zonse amakhala oculuka kuposa zilizonse zimene tingadzimane (Malaki 3:10; w16.04 7 ¶15)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Ni madalitso otani amene napeza cifukwa codzimana kuti nitumikile Yehova?’