Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Nehemiya Anali Kufuna Kutumikila Ena, Osati Kutumikilidwa

Nehemiya Anali Kufuna Kutumikila Ena, Osati Kutumikilidwa

Nehemiya sanaone udindo wake monga popezela phindu (Neh. 5:14, 15, 17, 18; w02 11/1 27 ¶3)

Nehemiya sanali kungoyang’anila nchito, koma anali kugwila nawo (Neh. 5:16; w16.09 6 ¶16)

Nehemiya anapempha Yehova kuti akam’kumbukile cifukwa ca cikondi cake codzimana (Neh. 5:19; w00 2/1 32)

Ngakhale kuti Nehemiya anali bwanamkubwa, sanayembekezele kuti anthu azimupatsa ulemu wapadela. Iye ni citsanzo cabwino kwa onse amene ali na maudindo komanso mautumiki ena mumpingo.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi nimaganizila kwambili zimene ningacitile ena kuposa zimene nifuna kuti ena anicitile?’