July 10-16
EZARA 7-8
Nyimbo 82 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Khalidwe la Ezara Linacititsa Kuti Yehova Alemekezeke”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Ezara 8:1—N’cifukwa ciyani Ayuda ambili ku Babulo sanafune kupita naye Ezara ku Yerusalemu? (w06 1/15 19 ¶10)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Ezara 8:21-36 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Wobwelelako: Kuvutika—1 Yoh. 5:19. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvela mafunso amene aonekela.
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Chulani na kukambilanako vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (Koma musaitambitse) (th phunzilo 4)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!, na kumuonetsa mmene phunzilo la Baibo limacitikila. (th phunzilo 11)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 15)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 50 mfundo 1-5 komanso vidiyo yakuti Tetezani Ana Anu, imene ili m’bokosi yakuti “Kodi Mudziŵa?”
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 134 na Pemphelo