Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Khalidwe la Ezara Linacititsa Kuti Yehova Alemekezeke

Khalidwe la Ezara Linacititsa Kuti Yehova Alemekezeke

Ezara analola Mawu a Mulungu kutsogolela mtima wake na khalidwe lake (Ezara 7:10; w00 10/1 14 ¶8)

Kudzela mwa Ezara, anthu ena anaona nzelu za Mulungu (Ezara 7:25; si 75 ¶5)

Cifukwa cakuti Ezara anadzicepetsa pamaso pa Mulungu, sanakayikile kuti Yehova adzamutsogolela na kum’teteza (Ezara 8:21-23; it-1 1158 ¶4)

Popeza kuti Ezara anaonetsa nzelu yaumulungu, mfumu inamupatsa maudindo aakulu. Mofanana na Ezara, tingabweletse citamando pa Yehova mwa khalidwe lathu

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi anthu amene si Mboni amanilemekeza cifukwa cakuti nimatsatila mfundo za Mulungu za makhalidwe abwino?’