July 17-23
EZARA 9-10
Nyimbo 89 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Zotulukapo Zowawa za Kusamvela”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Ezara 10:44—N’cifukwa ciyani ana anawacotsa pamodzi na amayi awo? (w06 1/15 20 ¶2)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Ezara 9:1-9 (th phunzilo 2)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Seŵenzetsani thilakiti yakuti Kodi Mavuto Adzathadi? poyambitsa makambilanowo. (th phunzilo 13)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muitanileni ku misonkhano, ndiyeno chulani na kukambilanako vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? (Koma musaitambitse) (th phunzilo 6)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 11 ndime yoyamba na mfundo 1-3 (th phunzilo 14)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Kumvela Kumatiteteza (2 Ates. 1:8): (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Kenako funsani omvela mafunso awa: N’ciyani cidzacitika nkhondo ya Aramagedo isanacitike?
Kodi timapindula bwanji pali pano cifukwa cokhala omvela?
Kodi pali kugwilizana kotani pakati pa Aramagedo na kukhala womvela?
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 50 mfundo 6-7 na cidule cake, mafunso obweleza, komanso colinga
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 133 na Pempelo