July 24-30
NEHEMIYA 1-2
Nyimbo 47 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Nthawi Yomweyo N’napemphela”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Neh. 2:4—Kodi iyi inali nthawi yoyamba pamene Nehemiya anapemphela za nkhaniyi? Nanga ife tiphunzilapo ciyani? (w86 2/15 25)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Neh. 2:11-20 (th phunzilo 2)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muuzeni za webusaiti yathu na kumusiyila kakhadi koloŵela pa jw.org. (th phunzilo 16)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mugaŵileni cofalitsa ca m’Thuboksi yathu. (th phunzilo 3)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 11 tumawu toyamba pa “Kumbani Mozamilapo” na mfundo 4 (th phunzilo 11)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Khala Bwenzi la Yehova—Kodi Yehova Amayankha Mapemphelo?: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Kenako, funsani omvela funso ili: Kodi vidiyo imeneyi itiphunzitsa ciyani za pemphelo?
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 51
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 102 na Pemphelo