Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

July 3-9

EZARA 4-6

July 3-9

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Musalowelele Nchito Yomanga Nyumba ya Mulungu”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Ezara 6:13—N’cifukwa ciyani mawu akuti “Kutsidya la Mtsinje” ni ocititsa cidwi? (w93 6/15 32 ¶3-5)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Ezara 4:8-24 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Kuvutika—Yak. 1:13. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvela mafunso amene aonekela.

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muuzeni za webusaiti yathu na kum’siyila kakhadi koloŵela pa jw.org. (th phunzilo 1)

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’fotokozeleni mmene phunzilo la Baibo limacitikila, na kum’patsa kakhadi kopemphela phunzilo la Baibo. (th phunzilo 9)

UMOYO WATHU WACIKHRITU