July 31–August 6
NEHEMIYA 3-4
Nyimbo 143 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Mumaona Kuti Nchito Yamanja si Yokuyenelelani?”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Neh. 4:17, 18—Kodi munthu angagwile bwanji nchito na dzanja limodzi? (w06 2/1 9 ¶1)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Neh. 3:15-24 (th phunzilo 2)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mukayamba, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 3)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Kambilanani mfundo za pa cikuto ca kumbuyo ca bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!, na kum’pempha kuti muziphunzila naye Baibo. (th phunzilo 12)
Nkhani: (Mph. 5) km 11/12 1—Mutu: Sangalalani Cifukwa Cakuti Mwagwila Nchito Mwakhyama. (th phunzilo 10)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Kuseŵenza na Mboni za Yehova: (Mph. 8) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Kenako funsani omvela funso ili: Malinga na vidiyo imeneyi, kodi khalidwe lathu kunchito lingacitile bwanji umboni?
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 7)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 52
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 29 na Pemphelo