Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

June 13-19

MASALIMO 38-44

June 13-19
  • Nyimbo 4 ndi Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Yehova Amathandiza Odwala”: (Mph. 10)

    • Sal. 41:1, 2—Odala ni anthu amene amacita zinthu moganizila anthu onyozeka (w15 12/15 24 ndime 7 CIN; w91 10/1 14 ndime 6 CN )

    • Sal. 41:3—Yehova amathandiza anthu okhulupilika amene ndi odwala (w08 9/15 5 ndime 12-13 CN)

    • Sal. 41:12—Ciyembekezo ca mtsogolo cingathandize odwala kupilila (w15 12/15 27 ndime 18-19 CN; w08 12/15 6 ndime 15 CN)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu (Mph. 8)

    • Sal. 39:1, 2—Tingasamale bwanji zokamba zathu? (w09 5/15 4 ndime 5 CN; w06 5/15 20 ndime 12 CN)

    • Sal. 41:9—Kodi zimene zinacitikila Davide zinakwanilitsidwa bwanji pa Yesu? (w11 8/15 13 ndime 5 CN; w08 9/15 5 ndime 11 CN)

    • Kodi kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ningagwilitsile nchito mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Sal. 42:6– 43:5

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) Galamukani! ya 2016 Na. 3 nkhani ya pacikuto

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Galamukani! ya 2016 Na. 3 nkhani ya pacikuto

  • Phunzilo la Baibulo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) Uthenga Wabwino phunzilo 2 ndime 4-5—Tsilizani mwa kukamba mau oonetsa kuti mufuna kutambitsa vidiyo ya pa jw.org yakuti, Kodi Mulungu Ali ndi Dzina?

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU

  • Nyimbo 128

  • Yang’ananibe Pamphotho!: (Mph. 15) Kukambilana. Tambitsani vidiyo ya pa jw.org yakuti Khala Bwenzi la Yehova—Yang’ananibe Pamphotho! (Nyimbo 24). (Pitani pa ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA) Ndiyeno kambilanani mbali yakuti, “Yelekezelani Mmene Umoyo Ulili Masiku Ano ndi Mmene Udzakhalila Mtsogolo.” (Compare: Life Now and in the Future) Seŵenzetsani mafunso otsatilawa: Ni masinthidwe abwanji amene adzacitika m’Paradaiso? Ni madalitso otani amene mufunitsitsa kukalandila? Nanga kuganizila kwambili pa ciyembekezo cimene muli naco kudzakuthandizani bwanji kupilila? —2 Akor. 4:18.

  • Phunzilo la Baibulo la Mpingo: (Mph. 30) ia mutu 17 ndime 14-22, ndi kubwelelamo pa tsa. 152

  • Kubwelelamo ndi Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)

  • Nyimbo 36 ndi Pemphelo