Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MASALIMO 38-44

Yehova Amathandiza Odwala

Yehova Amathandiza Odwala

Atumiki okhulupilika ayenela kudalila Yehova kuti awathandize akakumana ndi mavuto

41:1-4

  • Davide anadwala kwambili

  • Davide anali kucita zinthu moganizila anthu onyozeka

  • Davide sanayembekezele Yehova kuti amucilitse mozizwitsa, koma kuti amulimbikitse ndi kumucilikiza

  • Yehova anali kuona kuti Davide ni wokhulupilika