June 20-26
MASALIMO 45-51
Nyimbo 67 ndi Pemphelo
Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Yehova Sadzanyoza Munthu Wosweka Mtima”: (Mph. 10)
Sal. 51:1-4—Davide anakhudzidwa kwambili atazindikila kuti wacimwila Yehova (w93 3/15 10-11 ndime 9-13 CN)
Sal. 51:7-9—Davide anafunika kukhululukidwa ndi Yehova kuti akhalenso wacimwemwe (w93 3/15 12-13 ndime 18-20 CN)
Sal. 51:10-17—Davide anadziŵa kuti Yehova amakhululukila munthu wolapadi (w15 6/15 14 ndime 6 CIN; w93 3/15 14- 17 ndime 4-16 CN)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu (Mph. 8)
Sal. 45:4—Ni mfundo yofunika kwambili iti imene tifunika kuikila kumbuyo? (w14 2/1 10 ndime 11 CIN)
Sal. 48:12, 13—Kodi mavesi amenewa aonetsa kuti tili ndi udindo wotani? (w15 7/15 9 ndime 13 CIN)
Kodi kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?
Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ningagwilitsile nchito mu ulaliki?
Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Sal. 49:10–50:6
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) Galamukani! ya 2016 Na. 3 10-11
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Galamukani! ya 2016 Na. 3 10-11
Phunzilo la Baibulo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) Uthenga Wabwino phunzilo 3 ndime 1—Tsilizani mwa kukamba mau oonetsa kuti mufuna kutambitsa vidiyo ya pa jw.org yakuti, Ndani Analemba Baibulo?
UMOYO WATHU WACIKHIRISTU
“Ufumu wa Mulungu Wakwanitsa Zaka Zoposa 100”: (Mph. 15) Mafunso ndi mayankho. Yambani mwa kutambitsa vidiyo ya pa jw.org yakuti Ufumu wa Mulungu Wakwanitsa Zaka Zoposa 100. (The Kingdom—100 Years and Counting) Imani pa mbali yakuti, “An Education in One Day.” (Pitani pa MABUKU > MAVIDIYO.)
Phunzilo la Baibulo la Mpingo: (Mph. 30) ia mutu 18 ndime 1-13
Kubwelelamo ndi Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)
Nyimbo 109 ndi Pemphelo